Lonjezo Lakwaniritsidwa

Lonjezo Lakwaniritsidwa

Yesu anali atagwira ntchito ndi kuyenda ndi ophunzira ake kwa zaka zitatu, ndipo zinkawoneka ngati wafika ku mapeto a imfa yapa mtanda wosema, koma pa tsiku lachitatu Yesu anauka kwa akufa, naonekera kwa ophunzira ndi abwenzi ake, Iye an awalimbikitsa iwo kukhala pamodzi, ndi kuti asaike kwambiri pa zinthu zathupi angakhale ali muthupi la ulemerero), ndi kuyembekezera chinthu china.

Read More